Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 31:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 “Monga mmene ndakhalira ndikufunafuna mpata+ kuti ndiwazule, kuwagwetsa, kuwapasula, kuwawononga ndi kuwasakaza,+ ndidzakhalanso nawo tcheru kuti ndiwamange ndi kuwabzala,”+ watero Yehova.

  • Yeremiya 32:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 ‘Mzinda uwu wakhala chinthu chondikwiyitsa+ ndi chondipsetsa mtima kuyambira pamene unamangidwa kufikira lero. Choncho ndiuchotsa pamaso panga,+

  • Malaki 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kuyambira m’masiku a makolo anu mwakhala mukupatuka pa malamulo anga ndipo simunawasunge.+ Bwererani kwa ine ndipo ine ndibwerera kwa inu,”+ watero Yehova wa makamu.

      Koma inu mukunena kuti: “Tibwerere motani?”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena