Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 23:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Koma Yehova anati: “Yuda+ nayenso ndim’chotsa pamaso panga+ monga mmene ndinachotsera Isiraeli,+ ndipo ndithu ndidzakana ngakhale mzinda wa Yerusalemu umene ndinausankha, ndi nyumba imene ndinanena kuti, ‘Dzina langa lizikhala pamenepo.’”+

  • 2 Mafumu 24:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Zimenezi zinachitikira Yuda molamulidwa ndi Yehova, kuti achotse+ dzikolo pamaso pake chifukwa cha machimo a Manase,+ malinga ndi zonse zimene anachita,

  • Maliro 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Yerusalemu wachita tchimo+ lalikulu. N’chifukwa chake wakhala chinthu chonyansa.+

      Onse amene anali kumulemekeza ayamba kumuona ngati chinthu chachabechabe,+ chifukwa aona maliseche+ ake.

      Iyenso akuusa moyo+ ndipo watembenukira kwina chifukwa cha manyazi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena