Yeremiya 23:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndidzachititsa kuti mukhale ndi manyazi mpaka kalekale ndipo mudzanyozeka mpaka kalekale. Zimenezi sizidzaiwalika.”’”+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:40 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, ptsa. 12-13
40 Ndidzachititsa kuti mukhale ndi manyazi mpaka kalekale ndipo mudzanyozeka mpaka kalekale. Zimenezi sizidzaiwalika.”’”+