-
Yeremiya 24:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Anthu amene anatengedwa ku Yuda kupita ku ukapolo, amene ndinawachotsa mʼdziko lino nʼkuwatumiza kudziko la Akasidi ali ngati nkhuyu zabwino zimenezi. Ndidzawaona kuti ndi anthu abwino.
-