Yeremiya 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Anthu otengedwa ku Yuda kupita ku ukapolo kudziko la Akasidi ndidzawaona ngati nkhuyu zabwino zimenezi. Ndidzawatumiza kudziko la Akasidi+ kuchoka m’dziko lino m’njira yabwino.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:5 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, ptsa. 14-15, 17
5 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Anthu otengedwa ku Yuda kupita ku ukapolo kudziko la Akasidi ndidzawaona ngati nkhuyu zabwino zimenezi. Ndidzawatumiza kudziko la Akasidi+ kuchoka m’dziko lino m’njira yabwino.+