Yeremiya 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “‘Ndipo Yekoniya+ mwana wa Yehoyakimu,+ mfumu ya Yuda, ndiponso anthu onse a mu Yuda amene anatengedwa kupita ku ukapolo ku Babulo+ ndiwabwezeretsa kuno, chifukwa ndidzathyola goli la mfumu ya Babulo,’ akutero Yehova.”
4 “‘Ndipo Yekoniya+ mwana wa Yehoyakimu,+ mfumu ya Yuda, ndiponso anthu onse a mu Yuda amene anatengedwa kupita ku ukapolo ku Babulo+ ndiwabwezeretsa kuno, chifukwa ndidzathyola goli la mfumu ya Babulo,’ akutero Yehova.”