Yeremiya 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Pita ukauze Mfumu Zedekiya+ ya Yuda kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Ine ndikupereka mzindawu mʼmanja mwa mfumu ya Babulo ndipo idzauwotcha ndi moto.+
2 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Pita ukauze Mfumu Zedekiya+ ya Yuda kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Ine ndikupereka mzindawu mʼmanja mwa mfumu ya Babulo ndipo idzauwotcha ndi moto.+