Yeremiya 34:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iweyo adzakugwira ndithu nʼkukupereka kwa iye ndipo sudzathawa mʼmanja mwake.+ Udzaonana ndi mfumu ya Babulo maso ndi maso ndipo idzalankhula nawe. Iweyo udzapita ku Babulo.’+
3 Iweyo adzakugwira ndithu nʼkukupereka kwa iye ndipo sudzathawa mʼmanja mwake.+ Udzaonana ndi mfumu ya Babulo maso ndi maso ndipo idzalankhula nawe. Iweyo udzapita ku Babulo.’+