-
Yeremiya 34:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Choncho akalonga onse ndi anthu onse anamvera. Iwo anachita pangano kuti aliyense amasule akapolo ake aamuna ndi aakazi kuti asakhalenso akapolo. Iwo anamvera nʼkuwalola kuti achoke.
-