10 Choncho akalonga onse+ anamvera, chimodzimodzinso anthu onse amene anachita pangano kuti aliyense wa iwo alole wantchito wake wamwamuna kapena wamkazi kupita kwawo mwaufulu. Anamvera ndi kuwalola kuchoka kuti asawagwiritsenso ntchito monga atumiki awo.+