Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 26:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kenako akalonga a Yuda anamva mawu amenewa ndipo anakwezeka kuchokera kunyumba ya mfumu kupita kunyumba ya Yehova.+ Kumeneko anakhala pansi pachipata chatsopano cha nyumba ya Yehova.+

  • Yeremiya 36:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pamenepo anapita kunyumba ya mfumu, kuchipinda chodyera cha mlembi, kumene akalonga onse anali atakhala pansi. Kumeneko kunali Elisama+ mlembi, Delaya+ mwana wa Semaya, Elinatani+ mwana wa Akibori,+ Gemariya+ mwana wa Safani,+ Zedekiya mwana wa Hananiya ndi akalonga ena onse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena