2 Mafumu 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Hilikiya+ mkulu wa ansembe anauza Safani+ mlembi+ kuti: “Ndapeza buku la chilamulo+ m’nyumba ya Yehova!” Choncho Hilikiya anapereka bukulo kwa Safani, ndipo iye anayamba kuliwerenga. Yeremiya 26:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Ahikamu,+ mwana wa Safani+ anali kuteteza Yeremiya kuti anthu asamuphe.+ Yeremiya 39:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo anatuma anthuwo kuti akatenge Yeremiya m’Bwalo la Alonda+ ndi kumupereka kwa Gedaliya+ mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani,+ kuti apite naye kunyumba kwake, kuti Yeremiyayo akakhale pakati pa anthu akwawo.
8 Kenako Hilikiya+ mkulu wa ansembe anauza Safani+ mlembi+ kuti: “Ndapeza buku la chilamulo+ m’nyumba ya Yehova!” Choncho Hilikiya anapereka bukulo kwa Safani, ndipo iye anayamba kuliwerenga.
14 Iwo anatuma anthuwo kuti akatenge Yeremiya m’Bwalo la Alonda+ ndi kumupereka kwa Gedaliya+ mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani,+ kuti apite naye kunyumba kwake, kuti Yeremiyayo akakhale pakati pa anthu akwawo.