Yeremiya 26:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Mfumu Yehoyakimu inatumiza Elinatani, mwana wa Akibori+ ndi amuna ena ku Iguputo. Yeremiya 36:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ngakhale kuti Elinatani,+ Delaya+ ndi Gemariya+ anachonderera mfumu kuti isatenthe mpukutuwo, mfumuyo sinawamvere.+
25 Ngakhale kuti Elinatani,+ Delaya+ ndi Gemariya+ anachonderera mfumu kuti isatenthe mpukutuwo, mfumuyo sinawamvere.+