Yeremiya 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo inuyo posachedwapa* munasintha nʼkuchita zabwino pamaso panga polengeza ufulu kwa abale anu. Munachita pangano pamaso panga, mʼnyumba imene imatchulidwa ndi dzina langa.
15 Ndipo inuyo posachedwapa* munasintha nʼkuchita zabwino pamaso panga polengeza ufulu kwa abale anu. Munachita pangano pamaso panga, mʼnyumba imene imatchulidwa ndi dzina langa.