Yeremiya 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma inu munatembenuka ndi kuchita zolungama pamaso panga mwa kulengeza ufulu, aliyense kwa mnzake. Munachita pangano pamaso panga,+ m’nyumba imene ikutchedwa ndi dzina langa.+
15 Koma inu munatembenuka ndi kuchita zolungama pamaso panga mwa kulengeza ufulu, aliyense kwa mnzake. Munachita pangano pamaso panga,+ m’nyumba imene ikutchedwa ndi dzina langa.+