Yeremiya 34:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma kenako munasinthanso nʼkuipitsa dzina langa+ potenganso akapolo anu aamuna ndi aakazi amene munawalola kuti achoke nʼkupita kulikonse kumene anafuna. Inu munawakakamiza kuti akhalenso akapolo anu.’
16 Koma kenako munasinthanso nʼkuipitsa dzina langa+ potenganso akapolo anu aamuna ndi aakazi amene munawalola kuti achoke nʼkupita kulikonse kumene anafuna. Inu munawakakamiza kuti akhalenso akapolo anu.’