16 Kenako mwatembenukanso+ ndi kuipitsa dzina langa+ komanso aliyense wa inu watenganso wantchito wake wamkazi ndi wamwamuna amene munawalola kuchoka mwaufulu, zimenenso iwo anagwirizana nazo. Inu mwawatenganso kukhala antchito anu aamuna ndi antchito anu aakazi.’+