Yeremiya 36:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Tenga mpukutu ndipo ulembemo mawu onse amene ndakuuza okhudza chilango chimene ndidzapereke kwa Isiraeli, Yuda+ ndi mitundu yonse ya anthu.+ Ulembe mawu onse amene ndakuuza kuchokera nthawi imene ndinalankhula nawe mʼmasiku a Yosiya mpaka lero.+
2 “Tenga mpukutu ndipo ulembemo mawu onse amene ndakuuza okhudza chilango chimene ndidzapereke kwa Isiraeli, Yuda+ ndi mitundu yonse ya anthu.+ Ulembe mawu onse amene ndakuuza kuchokera nthawi imene ndinalankhula nawe mʼmasiku a Yosiya mpaka lero.+