Yeremiya 36:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno mʼchaka cha 5 cha ulamuliro wa Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, mʼmwezi wa 9, anthu onse a mu Yerusalemu ndi anthu onse amene anabwera ku Yerusalemu kuchokera mʼmizinda ya Yuda analengeza kuti asala kudya pamaso pa Yehova.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:9 Nsanja ya Olonda,8/15/2006, tsa. 17
9 Ndiyeno mʼchaka cha 5 cha ulamuliro wa Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, mʼmwezi wa 9, anthu onse a mu Yerusalemu ndi anthu onse amene anabwera ku Yerusalemu kuchokera mʼmizinda ya Yuda analengeza kuti asala kudya pamaso pa Yehova.+