-
Yeremiya 40:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Kenako Yohanani mwana wa Kareya anauza mwachinsinsi Gedaliya ku Mizipa kuti: “Ndikufuna ndipite kukapha Isimaeli mwana wa Netaniya ndipo palibe amene adziwe. Nʼchifukwa chiyani iyeyo akufuna kukupha? Nʼchifukwa chiyani akufuna kuti anthu onse a mu Yuda amene akubwera kwa iwe amwazike komanso kuti anthu amene anatsala mu Yuda awonongeke?”
-