-
Yeremiya 40:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ndiyeno Yohanani+ mwana wa Kareya anauza Gedaliya pamalo obisika ku Mizipa kuti: “Ndikufuna kupita tsopano lino kukapha Isimaeli mwana wa Netaniya pakuti palibe amene adzadziwa.+ N’chifukwa chiyani iyeyo akufuna kukupha? N’chifukwa chiyani akufuna kuti anthu onse a mu Yuda amene akubwera kwa iwe amwazike, ndi kuti anthu otsala mu Yuda awonongeke?”+
-