Yeremiya 42:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ‘Ngati mungakhalebe mʼdziko lino, ndidzakumangani osati kukugwetsani, ndidzakudzalani osati kukuzulani, popeza ndidzakumverani chisoni chifukwa cha tsoka limene ndakugwetserani.+
10 ‘Ngati mungakhalebe mʼdziko lino, ndidzakumangani osati kukugwetsani, ndidzakudzalani osati kukuzulani, popeza ndidzakumverani chisoni chifukwa cha tsoka limene ndakugwetserani.+