Yeremiya 42:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ‘Ngati mungakhalebe m’dziko lino,+ ndidzakulimbitsani osati kukupasulani, ndidzakubzalani osati kukuzulani,+ pakuti ndidzakumverani chisoni chifukwa cha tsoka limene ndakugwetserani.+
10 ‘Ngati mungakhalebe m’dziko lino,+ ndidzakulimbitsani osati kukupasulani, ndidzakubzalani osati kukuzulani,+ pakuti ndidzakumverani chisoni chifukwa cha tsoka limene ndakugwetserani.+