Yeremiya 44:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho ndinasonyeza mkwiyo wanga ndi ukali wanga ndipo unayaka mʼmizinda ya Yuda ndi mʼmisewu ya Yerusalemu moti mizinda imeneyi inakhala mabwinja komanso malo owonongeka ngati mmene zilili lero.’+
6 Choncho ndinasonyeza mkwiyo wanga ndi ukali wanga ndipo unayaka mʼmizinda ya Yuda ndi mʼmisewu ya Yerusalemu moti mizinda imeneyi inakhala mabwinja komanso malo owonongeka ngati mmene zilili lero.’+