Yeremiya 44:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho ndasonyeza mkwiyo wanga ndi ukali wanga ndipo watentha mizinda ya Yuda ndi misewu ya Yerusalemu.+ Lero malo amenewa ndi owonongeka ndipo asanduka bwinja.’+
6 Choncho ndasonyeza mkwiyo wanga ndi ukali wanga ndipo watentha mizinda ya Yuda ndi misewu ya Yerusalemu.+ Lero malo amenewa ndi owonongeka ndipo asanduka bwinja.’+