19 Akaziwo anawonjezera kuti: “Ndipo pamene tinkapereka nsembe ndi kuthira nsembe zachakumwa kwa Mfumukazi Yakumwamba, kodi amuna athu sanavomereze kuti tipangire Mfumukaziyo makeke oti tikapereke nsembe opangidwa mʼchifanizo chake ndiponso kuti tipereke kwa iye nsembe zachakumwazo?”