Yeremiya 44:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Komanso popereka nsembe zautsi ndi kuthira nsembe zachakumwa kwa ‘mfumukazi yakumwamba,’+ kodi sitinafunse amuna athu popangira mfumukaziyo mikate yopereka nsembe yopangidwa m’chifanizo chake kuti tipereke kwa iye nsembe zachakumwazo?”+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:19 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2156
19 “Komanso popereka nsembe zautsi ndi kuthira nsembe zachakumwa kwa ‘mfumukazi yakumwamba,’+ kodi sitinafunse amuna athu popangira mfumukaziyo mikate yopereka nsembe yopangidwa m’chifanizo chake kuti tipereke kwa iye nsembe zachakumwazo?”+