Yeremiya 44:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako Yehova sakanathanso kulekerera zinthu zoipa komanso zonyansa zimene munkachita ndipo dziko lanu linasanduka bwinja, chinthu chochititsa mantha ndi chotembereredwa, dziko lopanda munthu wokhalamo ngati mmene ziliri lero.+
22 Kenako Yehova sakanathanso kulekerera zinthu zoipa komanso zonyansa zimene munkachita ndipo dziko lanu linasanduka bwinja, chinthu chochititsa mantha ndi chotembereredwa, dziko lopanda munthu wokhalamo ngati mmene ziliri lero.+