28 Anthu ochepa okha adzathawa lupanga mʼdziko la Iguputo nʼkubwerera kudziko la Yuda.+ Ndipo pa nthawiyo, anthu amene anatsala mu Yuda amene anabwera mʼdziko la Iguputo kuti azikhalamo adzadziwa kuti mawu amene akwaniritsidwa ndi a ndani, mawu anga kapena mawu awo.”’”