Yeremiya 45:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Awa ndi mawu amene mneneri Yeremiya anauza Baruki+ mwana wa Neriya pa nthawi imene Baruki ankalemba mʼbuku mawu amene Yeremiya+ ankamuuza, mʼchaka cha 4 cha ulamuliro wa Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda. Yeremiya anati:
45 Awa ndi mawu amene mneneri Yeremiya anauza Baruki+ mwana wa Neriya pa nthawi imene Baruki ankalemba mʼbuku mawu amene Yeremiya+ ankamuuza, mʼchaka cha 4 cha ulamuliro wa Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda. Yeremiya anati: