-
Yeremiya 46:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ambiri akupunthwa ndi kugwa.
Iwo akuuzana kuti:
“Imirirani, tiyeni tibwerere kwa anthu a mtundu wathu ndi kudziko lathu
Chifukwa takumana ndi lupanga loopsa.”’
-