Yeremiya 47:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Yehova anauza mneneri Yeremiya mawu okhudza Afilisiti,+ Farao asanagonjetse mzinda wa Gaza.