-
Yeremiya 47:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Yehova wanena kuti:
“Taonani! Madzi akubwera kuchokera kumpoto.
Madzi ake adzakhala mtsinje wosefukira.
Ndipo adzakokolola dziko ndi zonse zimene zili mmenemo.
Adzakokololanso mzinda ndi onse amene akukhala mmenemo.
Amuna adzalira,
Ndipo aliyense amene akukhala mʼdzikolo adzalira mofuula.
-