Yeremiya 48:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Thawani, pulumutsani moyo wanu! Mukhale ngati mtengo wa junipa* mʼchipululu.