Yeremiya 48:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Thawani. Pulumutsani moyo wanu+ ndipo mukhale ngati mtengo umene uli wokhawokha m’chipululu.+