Yobu 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa cha njala ndiponso kusowa, iwo ali ngati akufa.Amatafuna dera lopanda madzi,+Limene dzulo kunali mphepo yamkuntho ndi chiwonongeko. Yeremiya 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Adzakhala ngati mtengo umene uli pawokhawokha m’chipululu ndipo zabwino zikadzafika sadzatha kuziona.+ Iye adzakhala m’malo ouma a m’chipululu m’dziko la nthaka yamchere, kumene sikukhala anthu.+
3 Chifukwa cha njala ndiponso kusowa, iwo ali ngati akufa.Amatafuna dera lopanda madzi,+Limene dzulo kunali mphepo yamkuntho ndi chiwonongeko.
6 Adzakhala ngati mtengo umene uli pawokhawokha m’chipululu ndipo zabwino zikadzafika sadzatha kuziona.+ Iye adzakhala m’malo ouma a m’chipululu m’dziko la nthaka yamchere, kumene sikukhala anthu.+