Yeremiya 50:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu a ku Isiraeli ali ngati nkhosa zomwazikana.+ Mikango ndi imene yawabalalitsa.+ Poyamba, mfumu ya Asuri inawadya.+ Kenako Mfumu Nebukadinezara* ya ku Babulo inakukuta mafupa awo.+
17 Anthu a ku Isiraeli ali ngati nkhosa zomwazikana.+ Mikango ndi imene yawabalalitsa.+ Poyamba, mfumu ya Asuri inawadya.+ Kenako Mfumu Nebukadinezara* ya ku Babulo inakukuta mafupa awo.+