Yeremiya 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Tsoka abusa amene akuwononga ndi kubalalitsa nkhosa zapamalo anga odyetsera ziweto!” akutero Yehova.+ Yeremiya 50:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu anga akhala ngati gulu la nkhosa zosochera.+ Abusa awo ndi amene anawasocheretsa.+ Anawatenga nʼkupita nawo mʼmapiri ndipo ankangowayendetsa kuchoka paphiri kupita pachitunda. Iwo aiwala malo awo opumulirako. Ezekieli 34:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho zinamwazikana chifukwa zinalibe mʼbusa+ ndipo zinakhala chakudya cha zilombo zonse zakutchire.
23 “Tsoka abusa amene akuwononga ndi kubalalitsa nkhosa zapamalo anga odyetsera ziweto!” akutero Yehova.+
6 Anthu anga akhala ngati gulu la nkhosa zosochera.+ Abusa awo ndi amene anawasocheretsa.+ Anawatenga nʼkupita nawo mʼmapiri ndipo ankangowayendetsa kuchoka paphiri kupita pachitunda. Iwo aiwala malo awo opumulirako.
5 Choncho zinamwazikana chifukwa zinalibe mʼbusa+ ndipo zinakhala chakudya cha zilombo zonse zakutchire.