Yeremiya 50:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti: ‘Ine ndilanga mfumu ya Babulo komanso dziko lake ngati mmene ndinalangira mfumu ya Asuri.+
18 Choncho Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti: ‘Ine ndilanga mfumu ya Babulo komanso dziko lake ngati mmene ndinalangira mfumu ya Asuri.+