Yeremiya 50:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ine ndikulanga mfumu ya Babulo ndi dziko lake ngati mmene ndinalangira mfumu ya Asuri.+
18 Choncho Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ine ndikulanga mfumu ya Babulo ndi dziko lake ngati mmene ndinalangira mfumu ya Asuri.+