Yeremiya 50:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Mʼmasiku amenewo ndiponso pa nthawi imeneyo,Cholakwa cha Isiraeli chidzafufuzidwa,Koma sichidzapezeka,” akutero Yehova.“Machimo a Yuda sadzapezeka,Chifukwa ine ndidzakhululukira anthu amene ndidzawasiye ndi moyo.”+
20 “Mʼmasiku amenewo ndiponso pa nthawi imeneyo,Cholakwa cha Isiraeli chidzafufuzidwa,Koma sichidzapezeka,” akutero Yehova.“Machimo a Yuda sadzapezeka,Chifukwa ine ndidzakhululukira anthu amene ndidzawasiye ndi moyo.”+