Maliro 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuti tipeze chakudya, timaika moyo wathu pachiswe+ chifukwa cha anthu amene ali ndi malupanga mʼchipululu.
9 Kuti tipeze chakudya, timaika moyo wathu pachiswe+ chifukwa cha anthu amene ali ndi malupanga mʼchipululu.