Ezekieli 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mngelo aliyense ankapita kutsogolo, ankapita kulikonse kumene mzimu ukufuna kuti apite.+ Angelowo sankatembenuka akamayenda.
12 Mngelo aliyense ankapita kutsogolo, ankapita kulikonse kumene mzimu ukufuna kuti apite.+ Angelowo sankatembenuka akamayenda.