Ezekieli 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chamoyo chilichonse chinkapita kutsogolo basi.+ Zamoyozo zinali kupita kulikonse kumene mzimu wafuna kuti zipite.+ Zikamayenda sizinali kutembenuka.+
12 Chamoyo chilichonse chinkapita kutsogolo basi.+ Zamoyozo zinali kupita kulikonse kumene mzimu wafuna kuti zipite.+ Zikamayenda sizinali kutembenuka.+