Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 103:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tamandani Yehova, inu angelo+ ake amphamvu, ochita zimene wanena,+

      Mwa kumvera malamulo ake.+

  • Ezekieli 1:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Kulikonse kumene mzimu ukufuna kupita, zamoyozo zinali kupita kumeneko, chifukwa mzimuwo wafuna kuti upite kumeneko. Mawilowo anali kukwera m’mwamba ali pambali pa zamoyozo, pakuti mzimu wa zamoyozo unali m’mawilowo.

  • Aheberi 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kodi angelo onse si mizimu+ yotumikira ena,+ yotumidwa kukatumikira amene adzalandire chipulumutso monga cholowa chawo?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena