Ezekieli 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Phokoso la mapiko awo linkamveka ngati phokoso la madzi omwe akuthamanga ndiponso ngati phokoso la Wamphamvuyonse.+ Angelowo akamayenda, ankamveka ngati phokoso la gulu la asilikali. Akaima, ankatsitsa mapiko awo pansi.
24 Phokoso la mapiko awo linkamveka ngati phokoso la madzi omwe akuthamanga ndiponso ngati phokoso la Wamphamvuyonse.+ Angelowo akamayenda, ankamveka ngati phokoso la gulu la asilikali. Akaima, ankatsitsa mapiko awo pansi.