-
Ezekieli 12:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ine ndinachita zonse zomwe anandilamula. Masana ndinatulutsa katundu wanga ngati katundu wopita naye ku ukapolo ndipo madzulo ndinabowola khoma ndi manja. Kutagwa mdima, ndinatulutsa katundu wanga ndipo ndinamunyamula paphewa iwo akuona.
-