Ezekieli 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Uthenga uwu ndi wokhudza mtsogoleri+ amene ali mu Yerusalemu ndi anthu onse a nyumba ya Isiraeli amene ali mumzindawu.”’
10 Uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Uthenga uwu ndi wokhudza mtsogoleri+ amene ali mu Yerusalemu ndi anthu onse a nyumba ya Isiraeli amene ali mumzindawu.”’