Ezekieli 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Pali uthenga uwu wotsutsana ndi mtsogoleri,+ uthenga wokhudza Yerusalemu ndi anthu onse a nyumba ya Isiraeli amene ali kumeneko.”’
10 Uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Pali uthenga uwu wotsutsana ndi mtsogoleri,+ uthenga wokhudza Yerusalemu ndi anthu onse a nyumba ya Isiraeli amene ali kumeneko.”’