-
Ezekieli 12:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Koma ndidzapulumutsa anthu ochepa pakati pawo kuti asaphedwe ndi lupanga, njala komanso mliri. Ndidzachita zimenezi kuti akafotokoze pakati pa anthu amitundu ina kumene adzapite zokhudza zinthu zonse zonyansa zimene ankachita ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”
-